Genesis 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mbiri ya Isaki mwana wa Abulahamu+ ndi iyi. Abulahamu anabereka Isaki.