Genesis 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele+ wa Chiaramu, wa ku Padani-aramu, amene anali mchemwali wake wa Labani wa Chiaramu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2137
20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele+ wa Chiaramu, wa ku Padani-aramu, amene anali mchemwali wake wa Labani wa Chiaramu.