-
Genesis 25:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Isaki ankachonderera Yehova mosalekeza zokhudza mkazi wake, chifukwa anali wosabereka. Choncho Yehova anamva pemphero lake, ndipo Rabeka mkazi wakeyo anakhala woyembekezera.
-