Genesis 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno ana amene anali mʼmimba mwake anayamba kulimbana,+ moti iye anati: “Ngati umu ndi mmene ndivutikire, kuli bwino ndingofa.” Choncho anafunsa Yehova kuti adziwe chifukwa chake.
22 Ndiyeno ana amene anali mʼmimba mwake anayamba kulimbana,+ moti iye anati: “Ngati umu ndi mmene ndivutikire, kuli bwino ndingofa.” Choncho anafunsa Yehova kuti adziwe chifukwa chake.