Genesis 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova anamuyankha kuti: “Mʼmimba mwako muli mitundu iwiri ya anthu+ ndipo mitundu iwiri imene idzatuluke mʼmimba mwako idzapita kosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamngʼono.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:23 Nsanja ya Olonda,1/15/2004, tsa. 2810/15/2003, tsa. 29 Kukambitsirana, tsa. 119
23 Yehova anamuyankha kuti: “Mʼmimba mwako muli mitundu iwiri ya anthu+ ndipo mitundu iwiri imene idzatuluke mʼmimba mwako idzapita kosiyana.+ Mtundu wina udzakhala wamphamvu kuposa mtundu winawo,+ ndipo wamkulu adzatumikira wamngʼono.”+