Genesis 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anyamatawa atakula, Esau anakhala mlenje waluso,+ munthu wokonda kuyenda mʼtchire. Koma Yakobo ankakonda kukhala mʼmatenti+ ndipo anali munthu wosalakwa. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:27 Nsanja ya Olonda,5/15/2013, tsa. 2710/15/2003, tsa. 28
27 Anyamatawa atakula, Esau anakhala mlenje waluso,+ munthu wokonda kuyenda mʼtchire. Koma Yakobo ankakonda kukhala mʼmatenti+ ndipo anali munthu wosalakwa.