Genesis 25:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndigawireko pangʼono mphodza zofiira zimene ukuphikazo,* ndatopatu ine!”* Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Edomu.*+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:30 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, tsa. 11
30 Ndiyeno Esau anapempha Yakobo kuti: “Chonde, fulumira ndigawireko pangʼono mphodza zofiira zimene ukuphikazo,* ndatopatu ine!”* Nʼchifukwa chake anamupatsa dzina lakuti Edomu.*+