Genesis 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero Yehova Mulungu anauza njokayo kuti:+ “Chifukwa cha zimene wachitazi, ukhala wotembereredwa pa nyama zonse zoweta ndi zakutchire. Udzakwawa ndi mimba yako ndipo udzadya fumbi masiku onse a moyo wako. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:14 Nsanja ya Olonda,6/15/2007, tsa. 318/1/1989, ptsa. 23-2412/15/1987, ptsa. 11-12
14 Zitatero Yehova Mulungu anauza njokayo kuti:+ “Chifukwa cha zimene wachitazi, ukhala wotembereredwa pa nyama zonse zoweta ndi zakutchire. Udzakwawa ndi mimba yako ndipo udzadya fumbi masiku onse a moyo wako.