-
Genesis 25:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Atatero Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya nʼkumwa. Kenako, ananyamuka nʼkumapita. Umu ndi mmene Esau anasonyezera kuti ankaona kuti ukulu wake unali wopanda phindu.
-