-
Genesis 3:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno Mulungu anauza mkaziyo kuti: “Ndidzawonjezera kwambiri kuvutika kwako pa nthawi imene uli woyembekezera. Ndipo pobereka ana udzamva ululu. Uzidzafunitsitsa kukhala ndi mwamuna wako, ndipo iye azidzakulamulira.”
-