Genesis 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamene atumiki a Isaki ankakumba zitsime mʼchigwacho,* anapeza chitsime cha madzi abwino.