-
Genesis 26:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Tichite pangano kuti sudzatichitira choipa chilichonse, chifukwa ifenso sitinakuchitire choipa chilichonse. Tinakuchitira zabwino zokhazokha, chifukwa tinakuuza kuti uchoke kwathu kuja mwamtendere. Ndipo panopa Yehova wakudalitsa.’”
-