Genesis 26:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsiku limenelo, atumiki a Isaki anapita kwa iye nʼkumuuza zokhudza chitsime chimene anakumba.+ Anamuuza kuti: “Ife tapeza madzi.”
32 Tsiku limenelo, atumiki a Isaki anapita kwa iye nʼkumuuza zokhudza chitsime chimene anakumba.+ Anamuuza kuti: “Ife tapeza madzi.”