Genesis 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Isaki anakalamba moti maso ake anasiya kuona. Ndiyeno anaitana mwana wake wamkulu Esau+ nʼkumuuza kuti: “Mwana wanga!” Iye anayankha kuti: “Ine bambo!”
27 Tsopano Isaki anakalamba moti maso ake anasiya kuona. Ndiyeno anaitana mwana wake wamkulu Esau+ nʼkumuuza kuti: “Mwana wanga!” Iye anayankha kuti: “Ine bambo!”