Genesis 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zimenezi, Adamu anapatsa mkazi wake dzina lakuti Hava,* chifukwa anali woti adzakhala mayi wa anthu onse.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:20 Nsanja ya Olonda,4/15/1999, tsa. 17
20 Pambuyo pa zimenezi, Adamu anapatsa mkazi wake dzina lakuti Hava,* chifukwa anali woti adzakhala mayi wa anthu onse.+