Genesis 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye sanamuzindikire, chifukwa manja ake anali acheya ngati manja a Esau mʼbale wake. Choncho anamudalitsa.+
23 Iye sanamuzindikire, chifukwa manja ake anali acheya ngati manja a Esau mʼbale wake. Choncho anamudalitsa.+