-
Genesis 27:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Iyenso anakonzera bambo ake nyama ija mopatsa mudyo. Kenako anapita nayo kwa bambo ake nʼkuwauza kuti: “Bambo, dzukani mudye nyama imene ine mwana wanu ndakupherani, kuti mundidalitse.”
-