Genesis 27:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Esau anafunsa bambo ake kuti: “Bambo, ngakhale dalitso limodzi silinatsaleko? Bambo ndidalitseni, inenso ndidalitseni chonde!” Atatero Esau analira mofuula kwambiri, misozi ili mbwembwembwe.+
38 Esau anafunsa bambo ake kuti: “Bambo, ngakhale dalitso limodzi silinatsaleko? Bambo ndidalitseni, inenso ndidalitseni chonde!” Atatero Esau analira mofuula kwambiri, misozi ili mbwembwembwe.+