Genesis 27:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pa nthawi yonse ya moyo wako uzidzadalira lupanga+ ndipo udzatumikira mʼbale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa mʼkhosi mwako.”+
40 Pa nthawi yonse ya moyo wako uzidzadalira lupanga+ ndipo udzatumikira mʼbale wako.+ Koma ukadzatopa ndi goli lake, udzalithyola ndi kulichotsa mʼkhosi mwako.”+