Genesis 27:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Rabeka atauzidwa zimene mwana wake wamkulu Esau ananena, nthawi yomweyo anaitanitsa mwana wake wamngʼono Yakobo nʼkumuuza kuti: “Mʼbale wako Esau akufuna akuphe pobwezera zimene unamuchitira.*
42 Rabeka atauzidwa zimene mwana wake wamkulu Esau ananena, nthawi yomweyo anaitanitsa mwana wake wamngʼono Yakobo nʼkumuuza kuti: “Mʼbale wako Esau akufuna akuphe pobwezera zimene unamuchitira.*