Genesis 27:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Izi zitachitika, Rabeka ankauza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Moyo wanga ndikunyansidwa nawo chifukwa cha akazi a Chihetiwa.+ Ngati Yakobo nayenso angatenge mkazi pakati pa akazi a Chiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:46 Nsanja ya Olonda,9/15/2006, ptsa. 21-227/15/1995, tsa. 138/1/1993, ptsa. 7-8
46 Izi zitachitika, Rabeka ankauza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Moyo wanga ndikunyansidwa nawo chifukwa cha akazi a Chihetiwa.+ Ngati Yakobo nayenso angatenge mkazi pakati pa akazi a Chiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+