Genesis 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Isaki anaitana Yakobo nʼkumudalitsa ndipo anamulamula kuti: “Usatenge mkazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:1 Nsanja ya Olonda,7/15/1995, tsa. 13
28 Ndiyeno Isaki anaitana Yakobo nʼkumudalitsa ndipo anamulamula kuti: “Usatenge mkazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+