Genesis 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Upite ku Padani-aramu kunyumba ya Betuele bambo a mayi ako. Kumeneko ukatenge mkazi pakati pa ana a Labani+ mchimwene wa mayi ako.
2 Upite ku Padani-aramu kunyumba ya Betuele bambo a mayi ako. Kumeneko ukatenge mkazi pakati pa ana a Labani+ mchimwene wa mayi ako.