Genesis 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakupatsa iwe ndi mbadwa* zako madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli, limene Mulungu anapatsa Abulahamu, lidzakhale lako.”+
4 Adzakupatsa iwe ndi mbadwa* zako madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli, limene Mulungu anapatsa Abulahamu, lidzakhale lako.”+