Genesis 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero Esau anazindikira kuti Isaki bambo ake ankanyansidwa ndi ana aakazi a ku Kanani.+