Genesis 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Esau anapita kwa Isimaeli* nʼkukatengako mkazi wina kuwonjezera pa akazi amene anali nawo. Mkaziyo dzina lake anali Mahalati ndipo anali mchemwali wake wa Nebayoti. Mahalati anali mwana wa Isimaeli, mwana wa Abulahamu.+
9 Choncho Esau anapita kwa Isimaeli* nʼkukatengako mkazi wina kuwonjezera pa akazi amene anali nawo. Mkaziyo dzina lake anali Mahalati ndipo anali mchemwali wake wa Nebayoti. Mahalati anali mwana wa Isimaeli, mwana wa Abulahamu.+