Genesis 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anayamba kulota. Mʼmalotowo anaona masitepe* ochokera padziko lapansi mpaka kumwamba, angelo a Mulungu akukwera ndi kutsika pamasitepewo.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:12 Nsanja ya Olonda,1/15/2004, tsa. 2810/15/2003, ptsa. 28-29
12 Kenako anayamba kulota. Mʼmalotowo anaona masitepe* ochokera padziko lapansi mpaka kumwamba, angelo a Mulungu akukwera ndi kutsika pamasitepewo.+