Genesis 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mbadwa zako ndithu zidzachuluka ngati mchenga wapadziko lapansi+ ndipo ana ako adzafalikira kumʼmawa, kumadzulo, kumpoto ndi kumʼmwera. Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbadwa zako, mabanja onse apadziko lapansi adzadalitsidwa ndithu.+
14 Mbadwa zako ndithu zidzachuluka ngati mchenga wapadziko lapansi+ ndipo ana ako adzafalikira kumʼmawa, kumadzulo, kumpoto ndi kumʼmwera. Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbadwa zako, mabanja onse apadziko lapansi adzadalitsidwa ndithu.+