Genesis 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndili ndi iwe. Ndikuyangʼanira kulikonse kumene ungapite ndipo ndidzakubwezera kudziko lino.+ Sindidzakusiya mpaka nditachita zimene ndakulonjeza.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2013, tsa. 21
15 Ine ndili ndi iwe. Ndikuyangʼanira kulikonse kumene ungapite ndipo ndidzakubwezera kudziko lino.+ Sindidzakusiya mpaka nditachita zimene ndakulonjeza.”+