Genesis 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Labani+ atangomva za Yakobo, mwana wa mchemwali wake, anathamanga kukakumana naye. Atafika, anamʼkumbatira ndi kumukisa nʼkupita naye kunyumba kwake. Ndipo Yakobo anafotokozera Labani zonse zimene zinamuchitikira.
13 Labani+ atangomva za Yakobo, mwana wa mchemwali wake, anathamanga kukakumana naye. Atafika, anamʼkumbatira ndi kumukisa nʼkupita naye kunyumba kwake. Ndipo Yakobo anafotokozera Labani zonse zimene zinamuchitikira.