Genesis 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamngʼonoyu.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:18 Nsanja ya Olonda,10/15/2003, tsa. 29
18 Koma Yakobo anakonda Rakele, ndiye anati: “Ndine wokonzeka kukugwirirani ntchito zaka 7, kuti mudzandipatse Rakele mwana wanu wamngʼonoyu.”+