Genesis 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele ndipo anamʼkonda kwambiri kuposa Leya, moti anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+
30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele ndipo anamʼkonda kwambiri kuposa Leya, moti anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+