Genesis 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Leya anakhala woyembekezera ndipo anabereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Rubeni,*+ ndipo anati: “Chifukwa Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:32 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 9
32 Choncho Leya anakhala woyembekezera ndipo anabereka mwana wamwamuna. Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Rubeni,*+ ndipo anati: “Chifukwa Yehova waona kusautsika kwanga,+ ndipo tsopano mwamuna wanga ayamba kundikonda.”