Genesis 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Levi.*+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:34 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 9
34 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Apa tsopano mwamuna wanga andikonda basi, chifukwa ndamuberekera ana aamuna atatu.” Choncho mwanayo anamupatsa dzina lakuti Levi.*+