Genesis 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anamupatsa mwanayo dzina lakuti Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anasiya kaye kubereka. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:35 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 9
35 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anamupatsa mwanayo dzina lakuti Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anasiya kaye kubereka.