Genesis 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi mchemwali wanga ndipo ndapambananso.” Choncho anapatsa mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:8 Nsanja ya Olonda,8/1/2002, ptsa. 29-30
8 Ndiyeno Rakele anati: “Ndalimbana mwamphamvu ndi mchemwali wanga ndipo ndapambananso.” Choncho anapatsa mwanayo dzina lakuti Nafitali.*+