Genesis 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanena kuti ndine wosangalala.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Aseri.*+
13 Mwanayo atabadwa, Leya anati: “Ndasangalala kwambiri! Akazi adzanena kuti ndine wosangalala.”+ Choncho Leya anapatsa mwanayo dzina lakuti Aseri.*+