Genesis 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Leya anakhalanso woyembekezera, moti patapita nthawi anaberekera Yakobo mwana wamwamuna wa 6.+