-
Genesis 4:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Utasintha nʼkumachita zinthu zabwino, kodi sindingayambirenso kusangalala nawe? Koma ngati susintha nʼkumachita zinthu zabwino, uchimo wakubisalira pakhomo, ndipo ukufunitsitsa kukumbwandira. Kodi iweyo suyesetsa kuti uwugonjetse?”
-