Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Kaini anauza Abele mʼbale wake kuti: “Tiye tipite kunkhalango.” Ali kunkhalangoko, Kaini anamenya Abele mʼbale wake nʼkumupha.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:8 Nsanja ya Olonda,1/1/2013, tsa. 159/15/2002, tsa. 28 Tsanzirani, tsa. 16
8 Kenako Kaini anauza Abele mʼbale wake kuti: “Tiye tipite kunkhalango.” Ali kunkhalangoko, Kaini anamenya Abele mʼbale wake nʼkumupha.+