Genesis 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo akayangʼana nkhope ya Labani ankaona kuti sakumuyangʼana ndi diso labwino ngati poyamba.+