Genesis 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anawauza kuti: “Ndikuona kuti bambo anu sakundiyangʼana ndi diso labwino ngati poyamba,+ koma Mulungu wa bambo anga sanandisiye.+
5 Iye anawauza kuti: “Ndikuona kuti bambo anu sakundiyangʼana ndi diso labwino ngati poyamba,+ koma Mulungu wa bambo anga sanandisiye.+