Genesis 31:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inunso mukudziwa bwino kuti bambo anu ndawagwirira ntchito ndi mphamvu zanga zonse.+