Genesis 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa nthawi imene ziweto zinali zokonzeka kutenga bere, ndinalota maloto ndipo ndinaona mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+
10 Pa nthawi imene ziweto zinali zokonzeka kutenga bere, ndinalota maloto ndipo ndinaona mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+