Genesis 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anapitiriza kuti, ‘Kweza maso ako ndipo uona kuti mbuzi zonse zamphongo zimene zikukwera zazikazizi ndi zamizeremizere, zamawangamawanga ndiponso zamathothomathotho. Ndachita zimenezi chifukwa ndaona zonse zimene Labani akukuchitira.+
12 Iye anapitiriza kuti, ‘Kweza maso ako ndipo uona kuti mbuzi zonse zamphongo zimene zikukwera zazikazizi ndi zamizeremizere, zamawangamawanga ndiponso zamathothomathotho. Ndachita zimenezi chifukwa ndaona zonse zimene Labani akukuchitira.+