Genesis 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atatero anayamba kutenga ziweto zake zonse ndi katundu wake yense amene anapeza+ ku Padani-aramu, nʼkunyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani kwa Isaki bambo ake.+
18 Atatero anayamba kutenga ziweto zake zonse ndi katundu wake yense amene anapeza+ ku Padani-aramu, nʼkunyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani kwa Isaki bambo ake.+