Genesis 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake, Rakele anaba aterafi*+ a bambo akewo.+