Genesis 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yakobo anathawa nʼkuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi anthu komanso katundu amene anali naye. Atatero analowera kudera la mapiri la Giliyadi.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2143
21 Yakobo anathawa nʼkuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi anthu komanso katundu amene anali naye. Atatero analowera kudera la mapiri la Giliyadi.+