Genesis 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atamva zimenezo, anatenga abale ake* nʼkuyamba kuthamangira Yakobo. Iwo anayenda ulendo wa masiku 7, ndipo anamupeza mʼdera la mapiri la Giliyadi.
23 Atamva zimenezo, anatenga abale ake* nʼkuyamba kuthamangira Yakobo. Iwo anayenda ulendo wa masiku 7, ndipo anamupeza mʼdera la mapiri la Giliyadi.