-
Genesis 31:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kenako Labani anapita kwa Yakobo. Pa nthawiyi nʼkuti Yakobo atamanga tenti yake mʼdera la mapiri la Giliyadi, ndipo Labani ndi abale ake anamanganso tenti yawo mʼdera lomwelo.
-